Mama Khadija Girls Academy 2020-21 form1 Intake

_______________________________________________________________________________
Bungwe la Al-Barakah Charity Trust likudziwitsa makolo ndi atsikana onse za mayeso olowera Form 1 kusukulu
ya Mama Khadija Girls Academy mchaka cha 2020/2021 motere:
TSIKU NDI NTHAWI BOMA/ DERA MALO
Loweruka
Pa
10 October, 2020
Nthawi ya
8:00 – 10:00 m’mawa
Nkhotakota Taaba Mosque
Kasungu Muhammad Mosque
Lilongwe Mchesi Madina Mosque
Thema Thema TDC
Makawa Hanafie Islamic Centre
Mzuzu Katoto Islamic Sec School
Zomba ZODEC
Liwonde Liwonde Main Mosque
Blantyre Kameza Training Centre
Namwera Mama Khadija Academy Hall
Dedza-Linthipe I Madina Mosque
Mangochi MADEC
Makanjira Mpiripiri F.P. School
Blantyre-Limbe Madina Central Mosque
Lamulungu
Pa
11 October, 2020
Nthawi ya
8:00 – 10:00 m’mawa
Salima Salima Main Mosque
Mponera (Dowa) Mponera Main Mosque
Namalweso Islamic Centre
Balaka Islamic Centre
Mchinji (boma) Banu Tambala Masjid
Mulanje Chitakale(Al-Barakah Offices)
Ntaja Ntaja CDSS
Ntakataka T/Off Abubakar Masjid
Ulongwe Kalembo Main Mosque
ZOFUNIKA
1. Chithunzi chimodzi cha passport atavala hijab.
2. Ophunzira aliyense adzapereka ndalama za mayeso zokwanira K3000.
3. Ophunzira abweretse cholembera, rula,calculator ndi ndalama zoyendera
pobwera kumalo a mayeso ndi popita kumudzi.
4. Ophunzira akhale wa zaka za pakati pa 13 ndi 15.
5. Ophunzira akhale amene walemba mayeso a Standard 8 a chaka cha 2020.
6. Musaiwale kutenga komanso kuvala masiki kuti tipewe corona.
Mukafuna kudziwa zambiri, imbirani a hedi pa nambala iyi : 01 586 000 nthawi ya ntchito.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *